Home Local News KUCHEZA_NDI_MIKE_WAWOH_ALIBEWAWOH

KUCHEZA_NDI_MIKE_WAWOH_ALIBEWAWOH

by Harris Msosa
216 views

Mike Wawoh Alibewawoh anabadwa pa 14 May 1986 ndipo m’banja mwawo mwana ndiyekha.

Mike anayamba kuyimba mu chaka cha 2000 ndipo adatulutsapo chimbale chake choyamba mu 2007 ndipo anadzayikhazikitsa ku Sheaffer mu mzinda wa Lilongwe.

Pakadali pano Mike ali mkati mojambula chimbale chake chatsopano chotchedwa Aliko Amamva chomwe akugwilira ntchito limodzi ndi Allan Chirwa,Barbra Nyangulu komanso Indonga.

Kupatula kuyimba Mike amagwira ntchito ngati Distribution komanso Logistics Manager ndi CKB Investments komanso amapanga business ndipo amakhala mu mzinda wa Blantyre.

kuwalagospelmusic.com is a Christian music website with all Malawian gospel music. For inquiries contact these numbers 0888 069 117/0983 592 032 or info@kuwalagospelmusic.com

All Rights Reserved – Designed and Developed by Kay Dee Media