Steven Kalonga ndi mlaliki pa mpingo wa New Life Christian Church amene amayimba nyimbo za uzimu kuchokera ku Mzimba koma kumudzi kochokera ndi ku Ntcheu. Mlaliki Steven adatulutsapo chimbale chimodzi …
Promise Dawe anayamba kuyimba mu chaka cha 2004 koma anayamba kuwonekera ku athu mu chaka cha 2021 ndipo anatulutsako chimbale chimodzi mu chaka cha 2023. “Ndimafuna ndidzakhale othandiza ma upcoming …
Alex Gomez K. Gondwe anayamba kuyimba mu chaka cha 2018 ndipo kufikira pano watulutsako ma single ake okwana awiri pamene nyimbo zake zina zitatu akuyembekezera kuzitulutsa mwezi wa mawa. “Ndinali …
Jolly Jack Chikaonda anabadwa pa 28 May, 1983 Ku mudzi kwawo ndi ku Luchenza (Municipal) boma la Thyolo,ndipo anayamba kuyimba kalekale cha m’ma 1998 koma kutulutsa nyimbo ngati oyimba wa …
Kelvin Maxwell anabadwa m’chaka cha 1994 ndipo m’banja lawo anabadwa ana asanu, amuna atatu, akazi awiri ndipo iye ndi wachinayi kubadwa. Kelvin anayamba kuyimba mu chaka cha 2006 koma kuyamba …
Mary Mhone anabadwa mu chaka cha 1988 ndipo m’banja mwawo anabadwa ana asanu ndipo iye ndi wachinayi kubadwa ndipo amakhala ku Pretoria dera lotchedwa Haertbeatsport Dam Schoemans Vill m’dziko la …
Emmanuel Liwotcha anabadwa pa 7 July, 1977 ndipo m’banja mwawo anabadwa ana 11 atsikana 4 ndi anyamata 7 ndipo pano anatsala anyamata 5 ndi atsikana atatu kamba koti enawo anamwalira …
Camillius Simakweri ndi mwana wachitatu kubadwa m’banja mwawo ndipo amakhala ku Mchinji Chipata Border.kumudzi kwawo ndi ku Chileka mu mzinda wa Blantyre koma anakhazikika ku Chilomoni. Camillius anayamba kuyimba mu …
Praise Nkwezalamba anabadwa pa 21 November, 1985 ndipo m’banja mwawo anabadwa ana 7, iye ndi wachitatu kubadwa ndipo amachokela m’mudzi mwa Nkoma pafupi ndi ku green corner mumzinda wa Blantyre. …
Mr Kazibweze Samuel Wilson was born in 1989 and they were born 8 children in their family and six are late. Mr Kazibweze started singing in 2017 and his first …