All Rights Reserved – Designed and Developed by Kay Dee Media
Author
Kuwala Gospel Music
Kuwala Gospel Music
kuwalagospelmusic.com is a Christian music website with all Malawian gospel music. For inquiries contact these numbers 0888 069 117/0983 592 032 or info@kuwalagospelmusic.com
Woodman Mussah – Moses
4 MB 5 Downloads
April 23, 2026
Joso Chimombo Gideon – Ndinu Nyali
17 MB 9 Downloads
April 9, 2026
Dan Mwananune Likhomo ndi mwana wa a muchose Likhomo omwe anachokela kwa Nasoko ku Phalombe,ndipo anachoka kumeneko nakazipezera malo ku Machinga m’mudzi wa Kwilasha pafupi ndi Malape.Dan M.Likhomo adabadwa m’chaka cha 1973.
Dan ndi mulomwe ndithu ndipo m’banja mwao anabadwamo ana 12 amuna 7 akazi 5 ndipo Dan ndi wa nambala 6 pakubadwa koma pano anatsala ana 8 akazi 4 amuna 4 ndipo ana 4 ndi makolo onse anamwalira.
Dan ndi munthu owopa Mulungu ndithu kuyambila ali m’nyamata komaso ofatsa ndipo alibe kudana ndi munthu.Dzina la Mwananune ndilozichepetsesa ndithu.
Dan anayamba kuyimba m’chaka cha 2003 ndipo wakhala nthawi yaitali osatulutsa chimbale kamba koyenda yenda koma nyimbo zinalibe zikuwila m’mutu mwake tsono pamene danga layamba kupezeka mpamene wayamba kutulutsa nyimbozi ndipo pano wajambulitsa kale nyimbo zosachepela 30 ndipo watenga nyimbo 15 kupanga chimbale chotchedwa Chiukitso volume 1 komaso vulume 2 ndiyojambulidwa kale.
Dan Mwananune Likhomo – Kodi Alipo
4 MB 6 Downloads
April 4, 2026
Dan Mwananune Likhomo – Tilira Kwanu
5 MB 7 Downloads
April 4, 2026
Dan Mwananune Likhomo – Akusambira
4 MB 10 Downloads
April 4, 2026
Dan Mwananune Likhomo – Jehova Wami
5 MB 17 Downloads
April 4, 2026
Dan Mwananune Likhomo – Oh Lord
6 MB 3 Downloads
April 4, 2026
Newer Posts