Home Local News KUCHEZA_NDI_NICE_NAKHARARI_(REX CHISONI NAKHARARI)

KUCHEZA_NDI_NICE_NAKHARARI_(REX CHISONI NAKHARARI)

by Harris Msosa
223 views

Nice Nakharari (Rex Chisoni Nakharari) anabadwa pa 7 July 1982 ndipo m’banja mwawo anabadwa ana 10 amuna 5, akazi 5 ndipo iye ndi wanamba 7 kubadwa.

Nice anayamba kuyimba mu chaka cha 2006 koma kupeka nyimbo anayamba mu 2000 ndipo pa 1 February Nice adatulutsa chimbale chake koma kutulutsa kowonekera kugula adatulutsa pa 8 April chomwe muli nyimbo 12 koma watulutsako ma singles mbuyomu ngati 2009 sizinamtole komanso Show me your love. Nice amakhala ku Dzenza Mission ku Area 25 mumzinda wa Lilongwe.

kuwalagospelmusic.com is a Christian music website with all Malawian gospel music. For inquiries contact these numbers 0888 069 117/0983 592 032 or info@kuwalagospelmusic.com

All Rights Reserved – Designed and Developed by Kay Dee Media