Home Local News KUMUDZIWA_ERNEST_THERERE

KUMUDZIWA_ERNEST_THERERE

by Harris Msosa
341 views

Ernest Therere anabadwa pa 27 May, 1997 ndipo m’banja mwawo anabadwa ana 6 anyamata 5 wamkazi m’modzi ndipo iye ndi oyamba kubadwa.

Ernest amakhala ku Chilomoni Kwanthukwa mumzinda wa Blantyre ndipo anayamba kuyimba mu chaka cha 2018.

“Ine kuyimba ndinayamba mu chaka cha 2014 ndimayimba mu choir ya Likhubula CCAP Sunday School koma nditazindikilitsidwa kuti ndingathe kuyimba ndipomwe ndinayamba kuyimba pandekha mu chaka cha 2018” adatero Enerst.

Zimbale zomwe Enerst watulutsako ndi ziwili yoyamba mutu wake Bwezi Langa ndi Yesu ndipo yachiwili ndi Lingalila za Yesu.

kuwalagospelmusic.com is a Christian music website with all Malawian gospel music. For inquiries contact these numbers 0888 069 117/0983 592 032 or info@kuwalagospelmusic.com

All Rights Reserved – Designed and Developed by Kay Dee Media