Home Local News KUMUDZIWA_MCDONALD_PHIRI (MCDONALD FUTURE)

KUMUDZIWA_MCDONALD_PHIRI (MCDONALD FUTURE)

by Harris Msosa
202 views

McDonald Phiri yemwe amadziwika bwino ndi dzina loti McDonald Future pamayimbidwe anabadwa pa 8 August , 1994 ndipo kwawo anabadwa ana 9 ndipo iye ndi wa chi 7 kubadwa.

McDonald anayamba kuyimba mu chaka cha 2020 koma kuyimba mokhazikika anayamba mu 2022 ndipo pakadali pano akukhalira m’dziko la South Africa.

kuwalagospelmusic.com is a Christian music website with all Malawian gospel music. For inquiries contact these numbers 0888 069 117/0983 592 032 or info@kuwalagospelmusic.com

All Rights Reserved – Designed and Developed by Kay Dee Media