Home Local News NYIMBO_ZANGA_ZINAYAMBA_KUBWELA_KU_MALOTO_NDITATEMBENUKA_MTIMA_KUMENE_2006 (GIVEN MULENGA)

NYIMBO_ZANGA_ZINAYAMBA_KUBWELA_KU_MALOTO_NDITATEMBENUKA_MTIMA_KUMENE_2006 (GIVEN MULENGA)

by Harris Msosa
192 views

Given Mulenga anabadwa pa 12 February m’chaka cha 1992 ndipo ndiwachiwiri kubadwa m’banja la ana atatu.

Kuyimba anayamba mu chaka cha 2018.watulutsapo chimbale chimodzi mutu wake “Chomwe Wadzala”.Choyamba nyimbo zanga zinayamba kubwera kumaloto nditatembenuka mtima kumene 2006 kenaka tinayamba choir yotchedwa Chaba Youth Assembless of God, kenaka kumayesela pa ndekha zinapezeka kuti zayamba kutheka kenaka ndinapanga chisakho chopita ku studio kuyamba kuyimba adatero Given.

Given amakhala ku dedza T/A chilikumwendo ndipo amagwira tchito ku Malawi Assembless of God Church ngati M’busa komaso ndi mlimi wa mbewu.

kuwalagospelmusic.com is a Christian music website with all Malawian gospel music. For inquiries contact these numbers 0888 069 117/0983 592 032 or info@kuwalagospelmusic.com

All Rights Reserved – Designed and Developed by Kay Dee Media