Mapulanga Francisco Vitsitsi was born on 16 June, 1979 at St Gabrielles Hospital in Lilongwe, Liwinga village Traditional Authority Kalolo,he is from a family of 8 and he is a …
All Rights Reserved – Designed and Developed by Kay Dee Media
Mapulanga Francisco Vitsitsi was born on 16 June, 1979 at St Gabrielles Hospital in Lilongwe, Liwinga village Traditional Authority Kalolo,he is from a family of 8 and he is a …
Albow Banda yemwe amadziwika bwino ndi dzina lakuti Albow B pamayimbidwe anabadwa mu chaka cha 1988 ndipo m’banja mwawo anabadwa ana anayi ndipo iye ndi oyamba kubadwa. Albow anayamba kuyimba …
Pastor Dr Maggie Maurice anabadwa pa 25 October, 1978 ndipo m’banja mwawo anabadwamo ana 6 ndipo iwo ndi omaliza koma ana atatu anamwalira ndipo anatsalanso atatu. Pastor Maurice anayamba kuyimba …
Middien Kanyika yemwe amadziwika bwino ndi dzina loti Middien 100% pa mayimbidwe anabadwa pa 10 October, 1992 ndipo m’banja mwawo anabadwa ana 8 ndipo iye ndi wa chi 7 kubadwa. …
McDonald Phiri yemwe amadziwika bwino ndi dzina loti McDonald Future pamayimbidwe anabadwa pa 8 August , 1994 ndipo kwawo anabadwa ana 9 ndipo iye ndi wa chi 7 kubadwa. McDonald …
Pastor Magret Nangwale anabadwa mu chaka cha 1982 ndipo m’banja mwawo anabadwa ana asanu ndipo iwo ndi achitatu kubadwa ndipo amakhala ku Chiladzulu. Pastor Nangwale anayamba kuyimba mu chaka cha …
Ernest Therere anabadwa pa 27 May, 1997 ndipo m’banja mwawo anabadwa ana 6 anyamata 5 wamkazi m’modzi ndipo iye ndi oyamba kubadwa. Ernest amakhala ku Chilomoni Kwanthukwa mumzinda wa Blantyre …
Montfort Jenala yemwe pamayimbidwe amadziwika ndi dzina lakuti MJ Monty anabadwa pa 12 April, 1985 ndipo m’banja mwawo anabadwa ana asanu ndipo iye ndi wachinayi kubadwa ndipo amakhala ku area …
John Masiye Ndaferankhande yemwe amadziwika ndi dzina loti John Fire pamayimbidwe anabadwa mu chaka cha 1987 ndipo m’banja mwawo anabadwa ana asanu ndipo iye ndi omaliza kubadwa. John anayamba kuyimba …
Pastor Maria Lemani Banda anabadwa pa 14 June 1985 ndipo m’banja mwawo anabadwa ana 10 ndipo iwo ndi achisanu kubadwa ndipo amakhala m’boma la Mwanza m’mudzi wa Chikorosa T/A Kanduku …
kuwalagospelmusic.com is a Christian music website with all Malawian gospel music. For inquiries contact these numbers 0888 069 117/0983 592 032 or info@kuwalagospelmusic.com
All Rights Reserved – Designed and Developed by Kay Dee Media