Home LyricsPraise Pemphero Kambela_Mwayenera_Lyrics

Praise Pemphero Kambela_Mwayenera_Lyrics

by Harris Msosa
1.1K views

Verse 1

Ndina sochela kutali,
Ine ndinadya ndi nguluwe,
Moyo wanga ine unatayika,
Koma Ambuye munandigwira dzanja.

Chorus

Mwayenela,
Mwayenela,
Mwayenela,
Ndinu chipulumutso changa.

Verse 2

Satana amakondwa,
Akandiona kuti ndagwa,
Popeza amadziwa
Kuti wagonjetsa,
Kwake ndi kuba, kupha ndi kuwononga.

Chorus
Mwayenela,
Mwayenela,
Mwayenela,
Ndinu chipulumutso changa.