Home Artist BiographyADA SIMEON CHIRWA – BIOGRAPHY.

ADA SIMEON CHIRWA – BIOGRAPHY.

by Kuwala Gospel Music
182 views

Ada Simeon Chirwa anabadwa mubanja la ana 5 ndipo iyeyo ndi wa chiwili.Anabadwa pa11,01,1988 koma ana onse akadali ndi moyo.Kumudzi kwawo ndiku nkhatabay,
Liuzi area, m’mudzi wa adamba liuzi. Anakwatilapo koma banja linatha
ndipo ali ndi mwana m’modzi yekha wamkazi dzina lake Midret Chirwa.Dzina lake lobadwa nalo ndi Simeon Chirwa koma anthu amangoti Ada Simeon Chirwa la pa music industry ndipo amapemphela mpingo wa Charismatic Redeemed Ministries International Church.

Pankhani ya mayimbidwe
Chinachitika kuti ayambe kuyimba nyimbo za uzimu ndi ichi
amakonda kwambili kuyimba nawo nyimbo za praise and worship ndipamene Panabwela ganizo loti ayambe kuyimba.Mu chaka cha 2020 anaimba nyimbo imodzi yomwe anthu ambili anayikonda kwambili
Ndikumupatsanso chilimbikiso kuti apitilizebe kuyimba ndipo nyimboyo mutu wake ndi Ukadzazindikila.