Home Local News KUCHEZA_NDI_PASTOR_PATRICK_MAKHUMULA

KUCHEZA_NDI_PASTOR_PATRICK_MAKHUMULA

by Kuwala Gospel Music
297 views

Pastor Patrick Makhumula anabadwa pa 11 October, 1979 ndipo m’banja mwawo anabadwa ana khumi,amuna asanu,akazinso asanu ndipo iwo ndi achitatu kubadwa. Pastor Makhumula amachokera ku Blantyre, ku Mdeka m’mudzi mwa a Nthache, T/A Chigaru koma pakadali pano akukhalira ku South Africa mumzinda wa Durban komwe akugwiranso ntchito.

Pastor Makhumula anayambila kuyimba ku Sunday School ndipo amakula ali muchimenecho ndipo kwa iwo mayimbidwe ndimayitanidwe.

Pastor Makhumula atulutsako nyimbo zatsopano zitatu mu mwezi wa March chaka chino monga Ndili pano, Mulinane komaso Ndidalira Inu.

kuwalagospelmusic.com is a Christian music website with all Malawian gospel music. For inquiries contact these numbers 0888 069 117/0983 592 032 or info@kuwalagospelmusic.com

All Rights Reserved – Designed and Developed by Kay Dee Media