Jack anayamba kuyimba m’ma 80’s mu kwaya ya Israel ya mpingo wa Soche CCAP ku Blantyre m’dera la mfumu Somba, kenako anayambitsanso gulu la kwaya ya Makata school ndipo anayamba kuyimba payekha nyimbo za uzimu mu chaka cha 1998 kufikira pano.
Cholinga chake ngati oyimba choyamba ndi utumiki omwe Mulungu anamupatsa kuti amutumikire pakusangalatsa,kuphunzitsa komanso kudziwitsa anthu za ufumu wake.Zokolola zamu utumiki umenewu amathandizira magawo ambiri mwachitsanzo za umoyo,maphunziro komanso za malimidwe ndikusamalira achikulire (Nkhalamba) ndi amasiye ndipo ngakhale Jack ali oyimba komanso amagwira ntchito.
2 comments
Awesome https://is.gd/tpjNyL
Awesome https://is.gd/tpjNyL