Victor Juma anabadwira ku Balaka, wakulira ku Mangochi kwa T/A Nakumba ndipo anabadwira mu banja la chikhristu.Mu banjamu alimo ana 8 ndipo iye ndi mwana wachitatu kubadwa ndipo iye anabadwa pa 17, August, 1991.
Victor amalemba ndikuyimba nyimbo ndipo
Timvelane ndi Yesu ndi nyimbo yake yoyamba ndipo iye ndi okwatira.