-
Chrispine Chaoneka nde dzina lake lapamsonkho koma lapa stage ndi EL DEEZ.Khili adabadwila ku Lilongwe, likuni hospital pa 18 February 1985 ndipo ndiwachiwili kubadwa m’banja la ana atatu.Oyamba kubadwa ndi …
-
Juliet Kunje Kazipeze anabadwira ku Bangwe mu mzinda wa Blantyre pa 10 March 1987, koma kumudzi kwawo ndi kwa Chitera ku Chiladzuru,ndipo m’banja mwawo anabadwa ana 4 iye ndi wa …
-
Platson Keliam Chammudzi anabadwa ndi kukulira ku Neno m’mudzi wa amtemankhawa T/A Dambe.Platson anabadwa pa 5 January,1994 ndipo m’banja mwawo anabadwa ana 8 anatsala amoyo 7 m’modzi adamwalira ndipo iye …
-
King William Chirwa Contacts:0996091516/0885606368 King William Chirwa Anabadwila ku Kasungu, Mtunthama trading center, T.A Wimbe. Anabadwa pa 18 January 1993 mu banja la ana 7 , anyamata 5 , atsikana …
-
Edward Filipo is a Malawian by nationality from Chewa tribe southern region of Malawi,Mangochi district.He was born in the family of 10 children,5 boys and 5 girls and he is …
-
Elisha Mbendera ndilo dzina lake lapa msonkho.Anabadwa mu chaka cha 1987 ndipo amakondwerera tsiku lakubadwa kwake pa 6 september. Anabadwa m’banja la Bambo ndi Mayi Mbendera pomwe anabereka ana okwana …
-
Clement Maungena “BK Boy” born on 12 September 1982 in Machinga district. He is from Balaka district, Batamila 2, T\A Nsamala. He is a Mechanical engineer and a musician and …
-
James Gulule ndi woimba,mtumiki (Evangelist) komanso mphunzitsi yemwe adabadwa pa 4 April,1992.Ndi mwana woyamba kubadwa m’banja la kwawo momwe muli ana 9 (amuna 4 ndipo akazi 5).Ndiokwatira ndipo ali ndi …
All Rights Reserved – Designed and Developed by Kay Dee Media