Middien kanyika (Middien 100%) Gospel artist was born in a Christian family of 8 and she is 7th and a born again Christian.She started singing when she was very little mu mpingo womwe her father was a Pastor.
Chifukwa chokonda kuimba sometimes she was running away from school kupita kuma training koma sizinamusokonezere maphunziro ake.
One day her Dad told her to stop singing and she refused ndipo she told him if you want me to stop singing then I will also stop going to your church and join another church so that I can get my freedom of singing
And she did stop going her father’s church and join CCAP church.
Analemba mayeso a standard 8 ndipo anakhoza bwino her father was so surprised and he believed her kuti kuimbaku sikungamusokonezeredi maphunziro but still she didn’t return to her father’s church and she became a full member of CCAP Church.Maphunziro ake anathera Form 4 Chifukwa chosowa school fees.
After a year she decided to join praise team ya pa church people mocked her moyo wake unafika powawa analibe friend oti she can call on her own she was very poor no good clothes nothing but still sanasiye kuimba mu praise team.
One day analota kuti ali pamwamba she was helping her friends kuti afike pomwe ali koma zimalephera kuti awathandize maloto awa amamulimbikitsa kuti in everything she is passing through she will still be somewhere poti ena sangafikire.
After a year she met this lovely lady Martha Nthakomwa.
She met Martha Nthakomwa ku function ya radio ABC in Mzuzu kunapezeka kuti amapemphera mpingo umodzi pa Chibavi CCAP Martha anamutenga kupita kukaimba kwina kwake after that anazamutengaso pokajambula nyimbo ya Kelvin Sato.
Tsiku lina anthuwa anaitanidwa ku festival ya choir kuti azayimbe at chibavi CCAP church atabwera she was with them kuwathandizira kuimba pa stage after service anthu anakumana oyimba ndikupanga chiganizo choti every English service adziyimba anali ma artist atatu Martha Nthakomwa,Kelvin Sato Komaso Lommey Ndovi she joined the team and analitcha group lija THE WORSHIPPERS.
Anthu anabwera kumawajoina ndipo anapanga team yayikulu kwambiri ena anayamba kutuluka because of ntchito amawapanga transfer but still after gulu litabwera chitonzo anachilandilanso chifukwanso sanali opeza bwino koma mu mtima wake nthawi zambiri samazitengera kwambiri amapitilirabe kuimba moyo kumapita.Atafika Potopa ndikunyozedwa anaganiza zoyambano kuimba payekha anatulutsa nyimbo koma inali yamadandaulo kwambiri anthu ambiri anamuunikira kuti asaitulutse chifukwa imachita kudziwikiratu kuti akuimba chifukwa chopsya mtima.
One day anakhala pansi kulingalira nyimbo yoti atulutse zinamuthera 2 years kuti akaitulutse nyimbo ya ZANGA ZILIBWINO nyimboyi anaimba misozi ikutuluka chifukwa mtima umawawa kuti angovomela kuti zonse zilibwino kaya anyozeke zonse za iye zilibwino.Anapita ku studio ya producer wina wake nyimbo siinatuluke bwino then anakhala pansi kuima kaye kuti azitolere kenako she decided to travel to south africa atafika ku south africa analembedwa ntchito ya m’nyumba bwana wake anali ovuta koma kuvuta kuja kunamupangitsa kuti awonjezereso zina mu nyimbo yake. One day abwana atachoka she decided to sing loud kuntchito ndipo after singing pompo anapanga record pompo and she decided to go ku studio kupita ku studio kupangidwaso chipongwe analuza ndalama koma anangolimba mtima kuti its okay let it be koma studio imeneyo anajambula nyimbo zonse 10 ndiye moyo unawawa analuza ndalama za nyimbo 10 she said to herself zonse zilibwino.She decided kupanga launch in 2018 in johannesburg kuti m’mene zilimo ngati ndikukonza azikonza imodzi imodzi and she did that.
When she came to holiday in 2018 anakumana ndi Steven Meleka yemwe anakambirana naye za project yake ndipo anamuuza zochita ndikuyamba kujambula. Album yake wajambula ma studio atatu, awiri sizinayende koma ya Steven Meleka (M STUDIOS) inamugwilira ntchito yokoma kwambiri mpaka pamwamba pa album anajambulanso ma singles awiri PEMPHERO komaso WANDITUMA YEHOVAH
Anthu amafunsa kodi Middien 100% linachokera pati?
Middien 100% pena amaliika kuti ndi music name koma kwakukulu 100% anabwera ndi zinthu zambiri zomwe wakhala akukumana nazo in her family and she use this name as stage name.Kuimba payekha anayamba chifukwa cha zambiri zomwe amakumana nazo anapanga chiganizo choimba payekha in 2014 ndipo in those days wakhala akukumana ndi oyimba ambiri ena amawathandizira backing kuma show.Chomwe chimamusangalatsa kwambiri mukuimba amakumana ndi anthu amsangala anthu opanda tsankho ndichomwe chimamupititsabe iye chitsogolo.