Ruth Chijani Zaipa anabadwa pa 24 May 1984, kwa bambo anabadwa ana awiri ndipo kwa mayi anabadwa ana asanu ndi m’modzi atsikana okhaokha ndipo konseku iye ndi oyamba kubadwa. Anayamba …
All Rights Reserved – Designed and Developed by Kay Dee Media
Ruth Chijani Zaipa anabadwa pa 24 May 1984, kwa bambo anabadwa ana awiri ndipo kwa mayi anabadwa ana asanu ndi m’modzi atsikana okhaokha ndipo konseku iye ndi oyamba kubadwa. Anayamba …
Costance Faith Kapanda anabadwa pa 19 September, 1994 ndipo m’banja mwawo anabadwa ana 4 ndipo iye ndi womaliza. Faith anayamba kuyimba m’chaka cha 2010 pamene adali ku sukulu ndipo pomufunsa …
Grace Kantwanje Kwilasi whose stage name is Grace Wokonderedwa was born in 1984 and released his first single in 2016. They are 7 in their family and she is number …
Rose Mwalure anabadwa mu chaka cha 1985 ndipo ndi mwana oyamba kubadwa m’banja lawo la ana anayi.Kumudzi kwawo ndi kwa Khayano T/A Nthilamanja boma la Mulanje.Kuyimba payekha anayamba mu chaka …
Patrick Simon Kangere anabadwa pa 11 May 1979 ndipo anayamba kuyimba mu chaka cha 1999. Mubanja mwawo anabadwa ana 9 atsikana atatu, anyamata 6 ndipo iwo ndi wa number 4. …
Nathan Simba anabadwa pa 28 June m’chaka cha 1989 lachitatu pa Chipatala cha Mangochi. Nathan anayamba kuyimba pakathawi zedi koma amkayimba mu choir ndipo analowa mu studio m’chaka cha 2019, …
Precious Walfred ndi m’modzi wa oyimba nyimbo zauzimu yemwe anabadwa pa 25 December m’chaka cha 1997. Precious wayamba kuyimba chaka chomwechino cha 2023 kudzela m’mayitanidwe a maloto.Precious watulutsa chimbale chake …
Lonnex Lawson Jeke Phiri anayamba kuyimba m’chaka cha 1993 pomwe anali ndi zaka 11. Mu chaka cha 2020 anatulutsa Album yotchedwa Ndiosunga moyo wanga. “Ndinayamba kuyimba chifukwa chosangalatsidwa ndi mayimbidwe …
Oyimba wina wa nyimbo za uzimu m’dziko muno yemwe amakhala ku Johannesburg m’dziko la South Africa Litah Lubano Nine watulutsa nyimbo yatsopano yotchedwa ndavomera lero. Nyimbo ya ndavomera yomwe ndiyabwino …
Oyimba odziwika bwino ndi nyimbo za uzimu m’dziko muno Henry Masamba watulutsa nyimbo yatsopano yotchedwa Levoz yomwe wayimba ndi mwana wake Moriah. Nyimboyi yajambulidwa ndi Macia ndipo ikukamba za ulemelero …
kuwalagospelmusic.com is a Christian music website with all Malawian gospel music. For inquiries contact these numbers 0888 069 117/0983 592 032 or info@kuwalagospelmusic.com
All Rights Reserved – Designed and Developed by Kay Dee Media