Oyimba nyimbo za uzimu otchuka m’dziko muno Khama Khwiliro watulutsa nyimbo yatsopano dzulo yotchedwa Testimony. Nyimbo yatsopanoyi ikukamba zoyamikira Mulungu komanso kuthokoza kuti chipanda Yesu m’nali chabe koma moyo wanga …
All Rights Reserved – Designed and Developed by Kay Dee Media
